Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu wawala ali ku Ziyoni,+ mzinda wokongola kwambiri.+ Zekariya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pa tsiku limenelo, Yehova Mulungu adzapulumutsa nkhosa zake,+ zimene ndi anthu ake.+ Pakuti iwo adzakhala ngati miyala yonyezimira ya pachisoti chachifumu m’dziko lake.+ 1 Atesalonika 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+
16 “Pa tsiku limenelo, Yehova Mulungu adzapulumutsa nkhosa zake,+ zimene ndi anthu ake.+ Pakuti iwo adzakhala ngati miyala yonyezimira ya pachisoti chachifumu m’dziko lake.+
19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?