Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 100:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+

      Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+

      Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+

  • Mika 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Iye adzaimirira n’kuyamba kuweta nkhosa mu mphamvu ya Yehova+ ndiponso m’dzina lalikulu la Yehova Mulungu wake.+ Anthuwo azidzakhala kumeneko motetezeka,+ pakuti iye adzakhala wamkulu mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Zekariya 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho ine ndinayamba kuweta nkhosa+ zimene zinayenera kuphedwa,+ ndipo ndinachita zimenezi chifukwa cha inu, anthu osautsika a m’gulu la nkhosali.+ Chotero ndinatenga ndodo ziwiri.+ Imodzi ndinaipatsa dzina lakuti Wosangalatsa.+ Inayo ndinaipatsa dzina lakuti Mgwirizano,+ ndipo ndinayamba kuweta gulu la nkhosalo.

  • Luka 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Musaope,+ kagulu ka nkhosa+ inu, chifukwa Atate wanu wavomereza kukupatsani ufumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena