Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+ Zekariya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Panganolo linasweka pa tsiku limenelo. Mwa njira imeneyi, nkhosa zosautsika+ zimene zinali kundiona+ zinadziwa kuti zimene ndachitazo n’zimene Yehova ananena.
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+
11 Panganolo linasweka pa tsiku limenelo. Mwa njira imeneyi, nkhosa zosautsika+ zimene zinali kundiona+ zinadziwa kuti zimene ndachitazo n’zimene Yehova ananena.