Yesaya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndiziyembekezera Yehova,+ amene wabisira nkhope yake nyumba ya Yakobo,+ ndipo ndithu ndiziyembekezera iyeyo.+ Luka 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.
17 Ine ndiziyembekezera Yehova,+ amene wabisira nkhope yake nyumba ya Yakobo,+ ndipo ndithu ndiziyembekezera iyeyo.+
25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.