Salimo 119:166 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 166 Ndayembekezera chipulumutso chanu, inu Yehova,+Ndipo ndatsatira malamulo anu.+ Yesaya 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Limbikitsani anthu anga. Ndithu alimbikitseni,” akutero Mulungu wanu anthu inu.+ Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+
13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+