Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 35:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu inu limbitsani manja ofooka ndiponso mawondo agwedegwede.+

  • Yesaya 49:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+

  • Yesaya 51:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti Yehova adzatonthoza Ziyoni.+ Iye adzatonthozadi malo ake onse owonongedwa.+ Adzachititsa chipululu chake kukhala ngati Edeni+ ndi dera lake lachipululu kukhala ngati munda wa Yehova.+ Mwa iye mudzakhala kusangalala ndi kukondwera, kuyamikira ndi kuimba nyimbo.+

  • Zekariya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova anayankha mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja. Anamuyankha ndi mawu abwino ndiponso olimbikitsa.+

  • 2 Akorinto 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atamandike Mulungu ndi Atate+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Tate wachifundo chachikulu+ ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena