Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 61:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 ndiponso kuti anthu onse amene akulirira Ziyoni ndiwapatse nsalu yovala kumutu m’malo mwa phulusa,+ ndiwapatse mafuta kuti azisangalala+ m’malo molira, ndiwapatse chovala choti azivala ponditamanda m’malo mokhala otaya mtima.+ Iwo adzatchedwa mitengo ikuluikulu ya chilungamo,+ yobzalidwa ndi Yehova+ kuti iyeyo akongole.+

  • Yeremiya 31:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Pa nthawi imeneyo, namwali, anyamata ndi amuna achikulire, onse pamodzi adzasangalala ndipo adzavina.+ Ndidzawachotsera chisoni chawo, moti kulira kwawo ndidzakusandutsa chisangalalo ndipo ndidzawatonthoza ndi kuwasangalatsa.+

  • 2 Atesalonika 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena