Yohane 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atate amalemekezeka mukapitiriza kubala zipatso zambiri ndi kusonyeza kuti mulidi ophunzira anga.+ 1 Akorinto 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+
20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+