Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba. Yohane 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mwakutero, onse adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga, ngati mukukondana.”+ Afilipi 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muchite zimenezi kutinso mudzazidwe ndi zipatso zolungama+ kudzera mwa Yesu Khristu, kuti Mulungu akalemekezedwe ndi kutamandidwa.+
16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba.
11 Muchite zimenezi kutinso mudzazidwe ndi zipatso zolungama+ kudzera mwa Yesu Khristu, kuti Mulungu akalemekezedwe ndi kutamandidwa.+