Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+ Yesaya 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Limbikitsani anthu anga. Ndithu alimbikitseni,” akutero Mulungu wanu anthu inu.+ Yesaya 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mofanana ndi munthu amene mayi ake amamutonthoza, inenso ndidzakutonthozani anthu inu,+ ndipo mudzatonthozedwa chifukwa cha Yerusalemu.+
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
13 Mofanana ndi munthu amene mayi ake amamutonthoza, inenso ndidzakutonthozani anthu inu,+ ndipo mudzatonthozedwa chifukwa cha Yerusalemu.+