Salimo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+ Salimo 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nanga tsopano, inu Yehova, ine ndikuyembekezera chiyani?Chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Aheberi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+ 2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+
12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+
9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+