Aroma 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale aulesi pa ntchito yanu.+ Yakani ndi mzimu.+ Tumikirani Yehova monga akapolo.+ Chivumbulutso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, ndakupeza ndi mlandu wakuti wasiya chikondi chimene unali nacho poyamba.+