Aheberi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muchite zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma muzitsanzira anthu amene, chifukwa cha chikhulupiriro ndiponso kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 16-17
12 Muchite zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma muzitsanzira anthu amene, chifukwa cha chikhulupiriro ndiponso kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza.