Aheberi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 16-17
12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+