Yesaya 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu a ku Ziyoni+ akadzabwerera n’kukakhala ku Yerusalemu,+ iwe sudzaliranso.+ Mosakayikira, iye adzakukomera mtima akadzamva kulira kwako. Akadzangomva kulira kwakoko, iye adzakuyankha.+ Aroma 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+
19 Anthu a ku Ziyoni+ akadzabwerera n’kukakhala ku Yerusalemu,+ iwe sudzaliranso.+ Mosakayikira, iye adzakukomera mtima akadzamva kulira kwako. Akadzangomva kulira kwakoko, iye adzakuyankha.+
4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+