Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 87:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ponena za Ziyoni anthu adzati:

      “Aliyense anabadwira mmenemo.”+

      Ndipo Wam’mwambamwamba+ adzakhazikitsa mzinda umenewo.+

  • Yesaya 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+

  • Yeremiya 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti tsiku lidzafika, pamene alonda amene ali m’mapiri a Efuraimu adzafuula kuti, ‘Nyamukani amuna inu, tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’”+

  • Zekariya 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Fuulanso kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mizinda yanga idzasefukira ndi zinthu zabwino.+ Yehova adzamva chisoni chifukwa cha tsoka limene anagwetsera Ziyoni+ ndipo adzasankhanso Yerusalemu.”’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena