Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Yesaya 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Yehova azidzayembekezera kuti akukomereni mtima+ ndipo adzanyamuka kuti akuchitireni chifundo,+ pakuti Yehova ndi Mulungu amene amaweruza mwachilungamo.+ Odala+ ndi anthu onse amene amamuyembekezera.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
18 Chotero Yehova azidzayembekezera kuti akukomereni mtima+ ndipo adzanyamuka kuti akuchitireni chifundo,+ pakuti Yehova ndi Mulungu amene amaweruza mwachilungamo.+ Odala+ ndi anthu onse amene amamuyembekezera.+