Salimo 102:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+ Aroma 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo, ndipo ndidzamvera chisoni aliyense amene ndikufuna kumumvera chisoni.”+
13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+
15 Pakuti iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo, ndipo ndidzamvera chisoni aliyense amene ndikufuna kumumvera chisoni.”+