Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Ezekieli 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzatembenukira kwa inu ndi kukuthandizani.+ Inu mapiri a ku Isiraeli, ndithu anthu adzalima minda mwa inu ndi kubzala mbewu.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
9 Ine ndidzatembenukira kwa inu ndi kukuthandizani.+ Inu mapiri a ku Isiraeli, ndithu anthu adzalima minda mwa inu ndi kubzala mbewu.+