Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Yeremiya 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Mudzaitanira pa ine komanso mudzabwera ndi kupemphera kwa ine ndipo ine ndidzakumvetserani.’+