28 Ndine amene ndikunena za Koresi+ kuti, ‘Iye ndi m’busa wanga ndipo adzakwaniritsa bwinobwino zonse zimene ndikufuna,’+ ngakhale zimene ndanena zokhudza Yerusalemu zakuti, ‘Adzamangidwanso,’ ndi zokhudza kachisi zakuti, ‘Maziko ako adzamangidwa.’”+