Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, Yehova analimbikitsa+ mtima wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa+ mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti:

  • Yesaya 41:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ine ndautsa winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+ Iye adzaitana pa dzina langa kuchokera kotulukira dzuwa.+ Adzaukira atsogoleri ngati kuti ndi dongo+ ndiponso ngati kuti iyeyo ndi woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.

  • Yesaya 45:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ine Yehova ndalankhula kwa wodzozedwa wanga.+ Ndalankhula kwa Koresi amene ndamugwira dzanja lake lamanja+ kuti ndigonjetse mitundu ya anthu pamaso pake,+ kuti ndimasule m’chiuno mwa mafumu, kuti ndimutsegulire zitseko zokhala ziwiriziwiri, moti ngakhale zipata sizidzatsekedwa. Ndalankhula kuti:

  • Yesaya 46:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+

  • Danieli 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa Koresi+ mfumu ya Perisiya, panali nkhani imene Danieli anauzidwa. Danieli ameneyu anali kutchedwa Belitesazara.+ Nkhani imene anauzidwayo inali yoona ndipo inali yokhudza nkhondo yaikulu.+ Danieli anamvetsa nkhani imeneyi ndiponso zinthu zimene anaona.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena