Nehemiya 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Alevi onse mumzinda woyera+ analipo 284. Yesaya 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti iwo amadzitcha kuti amakhala mumzinda woyera,+ ndipo amadalira Mulungu wa Isiraeli+ amene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Mateyu 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mdyerekezi anamutenga ndi kupita naye mumzinda woyera,+ ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi
2 Pakuti iwo amadzitcha kuti amakhala mumzinda woyera,+ ndipo amadalira Mulungu wa Isiraeli+ amene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+
5 Kenako Mdyerekezi anamutenga ndi kupita naye mumzinda woyera,+ ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi