Nehemiya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina. Yesaya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu zako+ iwe Ziyoni. Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera.+ Pakuti mwa iwe simudzabweranso munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa.+ Mateyu 27:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 ndi kuonekera kwa anthu ambiri. (Pambuyo pa kuukitsidwa kwa Yesu, anthu amene anali kuchokera kumanda achikumbutsoko, analowa mumzinda woyera.)+
11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina.
52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu zako+ iwe Ziyoni. Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera.+ Pakuti mwa iwe simudzabweranso munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa.+
53 ndi kuonekera kwa anthu ambiri. (Pambuyo pa kuukitsidwa kwa Yesu, anthu amene anali kuchokera kumanda achikumbutsoko, analowa mumzinda woyera.)+