Nehemiya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina. Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+ Mateyu 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mdyerekezi anamutenga ndi kupita naye mumzinda woyera,+ ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi
11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina.
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
5 Kenako Mdyerekezi anamutenga ndi kupita naye mumzinda woyera,+ ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi