Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho Yesuwa, Kadimiyeli, Bani, Hasabineya, Serebiya, Hodiya, Sebaniya ndi Petahiya, omwe anali Alevi, anati: “Dzukani, tamandani+ Yehova Mulungu wanu kuyambira kalekale mpaka kalekale.*+ Inu Mulungu wathu, anthuwa atamande dzina lanu laulemerero,+ lokwezeka kuposa dalitso ndi chitamando chilichonse.

  • Salimo 89:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+

      Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+

  • Salimo 145:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+

      Ndipo ukulu wake ndi wosasanthulika.+

  • Salimo 147:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+

      Nzeru zake zilibe malire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena