Yesaya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:1 Yesaya 2, ptsa. 180-182
52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+