-
Yesaya 35:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Munthu wodetsedwa sadzayenda mumsewu umenewo.+
Amene adzayendemo ndi munthu yekhayo amene ali woyenerera.
Palibe munthu wopusa amene adzayende mumsewu umenewo.
-
-
Yesaya 60:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.
Adzatenga dzikoli kukhala lawo mpaka kalekale.
-