Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Salimo 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+
40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+
5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+