Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+ Ezekieli 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo.+ Onse adzakhala ndi m’busa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga+ ndipo adzasunga malamulo anga+ ndi kuwatsatira.+
93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+
24 “‘“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo.+ Onse adzakhala ndi m’busa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga+ ndipo adzasunga malamulo anga+ ndi kuwatsatira.+