Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+ Ezekieli 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+
27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+