Salimo 133:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Taonani! Ndi zabwino komanso zosangalatsa kwambiriAbale akakhala pamodzi mogwirizana!+ Zekariya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndinatenga ndodo yanga yotchedwa Wosangalatsa+ ija ndi kuithyolathyola.+ Ndinachita izi kuti ndithetse pangano limene ndinapangana ndi anthu a mtundu wanga.+
10 Choncho ndinatenga ndodo yanga yotchedwa Wosangalatsa+ ija ndi kuithyolathyola.+ Ndinachita izi kuti ndithetse pangano limene ndinapangana ndi anthu a mtundu wanga.+