Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero Abulamu anauza Loti+ kuti: “Chonde, pasakhale mkangano uliwonse pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa abusa anga ndi abusa ako, pajatu ndife pachibale.+

  • Genesis 45:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Atatero, anauza abale akewo kuti anyamuke, ndipo iwo ananyamuka. Koma anawachenjeza kuti: “Musakanganetu m’njira.”+

  • Yohane 13:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mwakutero, onse adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga, ngati mukukondana.”+

  • Yohane 17:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+

  • Akolose 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma kuwonjezera pa zonsezi, valani chikondi,+ pakuti chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu+ kwambiri kuposa chinthu china chilichonse.

  • Aheberi 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mupitirize kukonda abale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena