Salimo 133:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Taonani! Ndi zabwino komanso zosangalatsa kwambiriAbale akakhala pamodzi mogwirizana!+ Miyambo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopsa mtima amayambitsa mkangano,+ koma munthu wosakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+ Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.