Yeremiya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+ Ezekieli 16:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Inenso ndidzakubwezera mogwirizana ndi zochita zako,+ chifukwa unanyoza lumbiro pophwanya pangano langa.+
21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+
59 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Inenso ndidzakubwezera mogwirizana ndi zochita zako,+ chifukwa unanyoza lumbiro pophwanya pangano langa.+