Yesaya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+ Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+
18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+
6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+