Deuteronomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani, Aisiraeli inu: Yehova Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.*+ 1 Mafumu 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthu onsewo ataona zimenezo, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ananena kuti: “Yehova ndiye Mulungu woona! Yehova ndiye Mulungu woona!” 2 Mafumu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ chonde tipulumutseni+ m’manja mwake, kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+ Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+
39 Anthu onsewo ataona zimenezo, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ananena kuti: “Yehova ndiye Mulungu woona! Yehova ndiye Mulungu woona!”
19 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ chonde tipulumutseni+ m’manja mwake, kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+