Miyambo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ananu, mverani malangizo* a bambo anu.+ Mvetserani kuti mupeze luso lomvetsa zinthu.+