Deuteronomo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka. Salimo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Bwerani kuno ana anga, ndimvetsereni.+Ndikuphunzitsani kuopa Yehova.+ Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, tamvera malangizo a bambo ako,+ ndipo usasiye malamulo a mayi ako,+ Miyambo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mvera uphungu+ ndipo utsatire malangizo* kuti udzakhale wanzeru m’tsogolo.+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+
7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.