Levitiko 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Miyambo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amatsegula pakamwa pake mwanzeru,+ ndipo lamulo la kukoma mtima kosatha lili palilime lake.+ 2 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti ndikukumbukira chikhulupiriro+ chopanda chinyengo+ chimene uli nacho, chimene chinayamba kukhazikika mwa agogo ako aakazi a Loisi, ndi mayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti chilinso mwa iwe. 2 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+
3 “‘Aliyense wa inu aziopa mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
5 Pakuti ndikukumbukira chikhulupiriro+ chopanda chinyengo+ chimene uli nacho, chimene chinayamba kukhazikika mwa agogo ako aakazi a Loisi, ndi mayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti chilinso mwa iwe.
15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+