Genesis 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Rabekayo anayankha kuti: “Eni, imwani mbuyanga.” Atatero anatsitsa mtsuko wake mwamsanga n’kuupendeketsa kuti mtumikiyo amwe.+ Yoswa 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 (Koma iye anali atawatengera padenga,*+ ndi kuwabisa pansi pa mapesi a fulakesi* padengapo.) 2 Mafumu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tiyeni tim’mangire kachipinda kapadenga*+ kukhoma.* M’kachipindamo timuikire bedi, tebulo, mpando, ndi choikapo nyale,+ kuti akabwera azikhala mmenemo.”+ Machitidwe 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+
18 Rabekayo anayankha kuti: “Eni, imwani mbuyanga.” Atatero anatsitsa mtsuko wake mwamsanga n’kuupendeketsa kuti mtumikiyo amwe.+
10 Tiyeni tim’mangire kachipinda kapadenga*+ kukhoma.* M’kachipindamo timuikire bedi, tebulo, mpando, ndi choikapo nyale,+ kuti akabwera azikhala mmenemo.”+
15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+