Oweruza 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ehudi anafika kwa mfumuyo ili yokhayokha m’chipinda chapadera chozizira bwino, chimene chinali padenga.* Pamenepo Ehudi anati: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu. 1 Mafumu 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Eliya anauza mayiyo kuti: “Bweretsa kuno mwana wakoyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo m’manja mwa mayi ake n’kupita naye kuchipinda chapadenga.+ Chipinda chimenechi n’chimene Eliya anali kukhalamo, ndipo anagoneka mwanayo pabedi lake.+
20 Ehudi anafika kwa mfumuyo ili yokhayokha m’chipinda chapadera chozizira bwino, chimene chinali padenga.* Pamenepo Ehudi anati: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu.
19 Koma Eliya anauza mayiyo kuti: “Bweretsa kuno mwana wakoyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo m’manja mwa mayi ake n’kupita naye kuchipinda chapadenga.+ Chipinda chimenechi n’chimene Eliya anali kukhalamo, ndipo anagoneka mwanayo pabedi lake.+