-
Machitidwe 9:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndipo m’masiku amenewo iye anadwala n’kumwalira. Choncho anamusambitsa ndi kumugoneka m’chipinda cham’mwamba.
-