Mateyu 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+ Aroma 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawanani ndi oyera malinga ndi zosowa zawo.+ Khalani ochereza.+ Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,+ pakuti potero, ena anachereza angelo mosadziwa.+
41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+