Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano anapitiriza kuwauza kuti: “Nyale saivundikira ndi dengu loyezera zinthu kapena kuiika pansi pa bedi, amatero kodi? Koma amaiika pachoikapo nyale, si choncho kodi?+
21 Tsopano anapitiriza kuwauza kuti: “Nyale saivundikira ndi dengu loyezera zinthu kapena kuiika pansi pa bedi, amatero kodi? Koma amaiika pachoikapo nyale, si choncho kodi?+