2 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mayiyo ananyamula mwanayo n’kukamugoneka pabedi+ la munthu wa Mulungu woona+ uja. Atatero anatuluka n’kutseka chitseko. 2 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Elisa analowa m’nyumbamo ndipo anapeza mwana wakufayo atam’goneka pabedi lake lija.+
21 Ndiyeno mayiyo ananyamula mwanayo n’kukamugoneka pabedi+ la munthu wa Mulungu woona+ uja. Atatero anatuluka n’kutseka chitseko.