2 Mafumu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tiyeni tim’mangire kachipinda kapadenga*+ kukhoma.* M’kachipindamo timuikire bedi, tebulo, mpando, ndi choikapo nyale,+ kuti akabwera azikhala mmenemo.”+
10 Tiyeni tim’mangire kachipinda kapadenga*+ kukhoma.* M’kachipindamo timuikire bedi, tebulo, mpando, ndi choikapo nyale,+ kuti akabwera azikhala mmenemo.”+