Mateyu 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha m’kapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pang’ono.”+ Mateyu 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pakuti ine ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya.+ Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+
42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha m’kapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pang’ono.”+
35 Pakuti ine ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya.+ Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+