Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+ Ezekieli 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sanazunzepo munthu aliyense.+ Sanatengepo chikole+ ndipo sanalandepo chilichonse mwauchifwamba.+ Munthu wanjala amam’patsa chakudya+ ndipo munthu wamaliseche amam’phimba ndi chovala.+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
16 Sanazunzepo munthu aliyense.+ Sanatengepo chikole+ ndipo sanalandepo chilichonse mwauchifwamba.+ Munthu wanjala amam’patsa chakudya+ ndipo munthu wamaliseche amam’phimba ndi chovala.+