Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako amuna amene anachita kusankhidwa powatchula mayina+ ananyamuka n’kutenga anthu ogwidwawo. Anthu onse amene sanavale* zovala anawaveka zovala+ zimene anafunkha ndipo anawavekanso nsapato. Anawapatsa chakudya+ ndi zakumwa,+ ndipo anawadzoza mafuta. Kuwonjezera apo, aliyense amene anali kuyenda movutikira anamukweza+ pabulu. Atatero anatenga anthuwo n’kupita nawo ku Yeriko,+ kumzinda wa mitengo ya kanjedza,+ kufupi ndi abale awo. Pambuyo pake iwo anabwerera ku Samariya.+

  • Ezekieli 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ngati sazunza munthu aliyense,+ ngati amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ ngati salanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati amapatsa munthu wanjala chakudya+ ndi kuphimba munthu wamaliseche ndi chovala,+

  • Mateyu 25:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’

  • Yakobo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngati m’bale kapena mlongo ali waumphawi ndipo alibe chakudya chokwanira pa tsikulo,+

  • 1 Yohane 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena